South Lunzu Youth Friendly Health Services

South Lunzu Youth Friendly Health Services is a Youth Organization Established by self mobilized young people and we are based at South Lunzu Health Centre in Machinjiri. Blantyre

South Lunzu Youth Friendly Health Services  LACHINAYI pa18 June 2026Kuzayaka mot🔥Ife achinyamata a Bungwe la  Active You...
02/06/2026

South Lunzu Youth Friendly Health Services
LACHINAYI pa
18 June 2026
Kuzayaka mot🔥

Ife achinyamata a Bungwe la
Active Youth Association
Tizalandira ALENDO
Achinyamata kuchokera ku NJULI m'boma la Chiradzulu a Bungwe la
TIKONDANE YOUTH & DRAMA CLUB

Kuzacheza ndiife achinyamata aku Blantyre

LACHINAYI limeneri kuzabebatu🔥🔥

Tizakhala ndi zochitika zambiri

Kusinthana Stage
Kuonetsana ZISUDZO
Kuti Blantyre ndi Chiradzulu amatha ndani...

Kuimba, ndakaturo ndi zina zambiri

Achinyamata akuno ku MACHINJIRI tonse
Tizabwere tizaibebese
Kuipatsa Mot🔥🔥🔥

H🫶art to  H🫶art Union is designed for individuals seeking serious relationships, offering a platform to connect souls an...
07/05/2026

H🫶art to H🫶art Union
is designed for individuals seeking serious relationships, offering a platform to connect souls and find lasting love.

💝 Pezani wa Chikondi wanu ❤️

Ndi K10,000 yokha
M***a kupeza Wachikondi wanu wa pa mtima muno
Mamuna/Mkadzi wa Banja Lachikondi

Tumizani uthenga ofuna Bwenzi kapena Banja ku
*0 995 690 336*
(Whatsapp/ Text)

"Where Souls Connect and True Love Finds Forever"

🤝JOIN WHATSAPP GROUP

https://chat.whatsapp.com/FF9HrwaGjQ3BUQTeizhhF7?mode=gi_t

07/05/2026

H🫶art to H🫶art Union
is designed for individuals seeking serious relationships, offering a platform to connect souls and find lasting love.

💝 Pezani wa Chikondi wanu ❤️

Ndi K10,000 yokha
M***a kupeza Wachikondi wanu wa pa mtima muno
Mamuna/Mkadzi wa Banja Lachikondi

Tumizani uthenga ofuna Bwenzi kapena Banja ku
*0 995 690 336*
(Whatsapp/ Text)

"Where Souls Connect and True Love Finds Forever"

🤝JOIN WHATSAPP GROUP

For Booking:0 888 878 678(Whatsapp / Call)
27/04/2026

For Booking:
0 888 878 678
(Whatsapp / Call)

TITHANDIZENI NDI ZOCHEPA ZOMWE MULI NAZO,ULENDO WOKACHEZA NDI AMAYI OYEMBEKEZERA:Okondedwa anzanthu inu, amtima wabwino ...
14/04/2026

TITHANDIZENI NDI
ZOCHEPA ZOMWE MULI NAZO,
ULENDO WOKACHEZA NDI AMAYI OYEMBEKEZERA:

Okondedwa anzanthu inu, amtima wabwino ndi ofunira zabwino

Ife a Bungwe la Mphatso the Gift Foundation , timakhulupirira kuti Mwana aliyense ndi m'dalitso, ndipo Mayi aliyense akuyenera kuthandizidwa ndi kulemekezedwa—makamaka pa nthawi ya msautso.

Monga bungwe lachifundo lachikhristu lokhazikika pa chikhulupiliro, lodzipereka kuthandiza ana amasiye, ana osauka, komanso okalamba, timadziwa kuti kuthyola unyolo wa umphawi kumayambira pomwe moyo umayamba.

Pa 4 July 2026, ku Machinjiri mu mzinda wa Blantyre,
Bungwe lathu la Mphatso the Gift Foundation tikupita pa chipatala cha
South Lunzu
(ku Maternity Ward),
Kukacheza ndi kukapereka 'Mphatso ya Chiyembekezo' kwa amayi a oyembekezera ndi omwe angobeleka kumene.

Tsiku li tizapeleka mphatso zosiyanana monga:
Zitenje, Mabeseni, mabigiliri, Sopo wosambira komanso wochapila, Sugar, matches, makandulo, ndi zina zofunikira.

Mphatso zi tikuzapeleka ngati njira imodzi ya uthenga wachikondi, wosonyeza amayi olimba mtima awa kuti sali okha ayi, sanaiwalike,

Tikupita m'chipinda cha amayi obereka (maternity ward)
kuti tikapereke chitonthozo kwa omwe akukumana ndi kufika kwa moyo watsopano ndi kusadziwa kapena mantha

Ife a Bungwe la Mphatso the Gift Foundation
Tikupempha chithandizo kwa inu nonse akufuna kwabwino ndi omvetsetsa ntchito za chifundo kuti mutithandize potigulira zinthu zomwe zatchulidwazi,
M***a kutithandiza ndi ndalama iliyonse yomwe mungathe Kuti ntchito ikwanilitsidwe komanso izayende bwino

Lowani nawo m'gulu lathu paulendo wokayankhula mawu olimbikitsa ndikufalitsa uthenga wabwino wa chikondi pa chipatala chi
(1 Akorinto 13:1-13)

KUTI MUTHANDIZE:


9100004034578
(Mphatso Limbanga)
Blantyre Branch


+265893232710
(Mphatso Limbanga)


+265995690336
(Mphatso Limbanga)

kuti mumve zambiri zokhuza ntchito ya chifundo yi imbani phone pa
+265 888 878 678
Blantyre, Malawi

Luke 10:25-37 and 1 Corinthians 13:1-13 :  As a faith-based community, we believe in surrounding new life with love. Mph...
10/04/2026

Luke 10:25-37 and 1 Corinthians 13:1-13

:

As a faith-based community, we believe in surrounding new life with love.

Mphatso the Gift Foundation is honored to announce our upcoming visit to the South Lunzu Health Centre Maternity Ward.
We will be blessing expectant mothers—particularly those facing hardship—with essential baby gifts and prayer.

We are reaching out to help vulnerable new lives and support our elderly in the community.

WE NEED YOUR HELP:
👏We are accepting donations of baby items or Funds to buy supplies

or Volunteering to JOIN our visiting team.

Let’s be the hands and feet of Christ. Together, we can make a difference.

For more information or Donation
+265 888 878 678
+265 990 135 224
(Whatsapp / Call)
Blantyre, Malawi

"

Donate, Support and Join the Movement
04/04/2026

Donate, Support and Join the Movement

Address

Active Youth Association. We Are Situated At South Health Centre. Machinjiri Area 2
Blantyre
P/BAG.66BLANTYRE

Telephone

+265888878678

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when South Lunzu Youth Friendly Health Services posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share