Farmer With A pproach ac

Farmer With A pproach ac Welcome to my official business page,

Chicken famer 🐣 🐀 🐀 πŸ₯
Pig farmer πŸ–πŸ–πŸ·πŸ·

Contact us on 0995369209
Call or whatsApp πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

zik*theka
18/03/2026

zik*theka

muweti samafooka ai apa mumawa Uno kukagula feed yowonjezela kunkhuku xathu
04/03/2026

muweti samafooka ai apa mumawa Uno kukagula feed yowonjezela kunkhuku xathu

mwini wake khola lino ndi amaneneyi πŸ“πŸ”πŸ˜‚πŸ˜‚
27/02/2026

mwini wake khola lino ndi amaneneyi πŸ“πŸ”πŸ˜‚πŸ˜‚

26/02/2026

kuzipasa chakudya

local chickenπŸ“ πŸ”
26/02/2026

local chickenπŸ“ πŸ”

uwu ndi ulendo wanga wa ulimi wa nkhuku za local ndauyamba motele
24/02/2026

uwu ndi ulendo wanga wa ulimi wa nkhuku za local ndauyamba motele

moikila nkhuku umu tankhoza apapa
24/02/2026

moikila nkhuku umu tankhoza apapa

nkhuku zimakonda kugona mumwamba pasi sizikondapo nde tinazipangila makwelelo awa k*t zizigonapo apa zose ndi izi
20/02/2026

nkhuku zimakonda kugona mumwamba pasi sizikondapo nde tinazipangila makwelelo awa k*t zizigonapo apa zose ndi izi

mwayendelako ku munda wa chimanga ngt?
20/02/2026

mwayendelako ku munda wa chimanga ngt?

siku loyamba k*tolela mazila pamene nkhuku zathu zayamba kuyikila πŸ₯°πŸ₯°πŸ₯°ndichiyambi ichi osafowoka
20/02/2026

siku loyamba k*tolela mazila pamene nkhuku zathu zayamba kuyikila πŸ₯°πŸ₯°πŸ₯°ndichiyambi ichi osafowoka

Address

P, O , BOX 4 CHAMPHILA
Jenda Theo

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Farmer With A pproach ac posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share