15/06/2026
* JATROPHA*
Chonde mveseseni ngati mubwere ku inbox mubwere ngati mukufuna kuzagula nawo. Koma ntchito yake ndi imeneyo
Follow Frank Wa Zachilengedwe
👇👇👇👇👇
☑️Mtengo umeneu umatchedwa Jatropha Nde pali red jatropha komaso green Jatropha .
☑️Kusiyanaku kumabwela kamba ka mtundu kapena kuti colour ya plant yakeyo
☑️Now azakafuku fuku atapanga adapeza kuti leaf extract ya mtengou uli Ndi mphamvu yothandiza ku matenda a HIV.
☑️komaso Umachiza matenda aja a candida
☑️kkmaso khungwa lake madzi ake amathandiza kuchiza malungo komaso zotupa zosiyana siyana
☑️Juice uyuyu wakhungwali kumuzoleka munthu wa mphere zimatha zose ,matuza amoto amapola komaso kupaka zipere zimapola.
☑️khungwa lakeli la fresh kuika nkamwa nkumatafuna KWA maola angapo limachiza matenda kutupa kea ausinini komwe kumapangisa kutupa nkamwa nkumatuluka mafinya.
☑️kmaso masamba ake kusinja nkumasamba komaso kupanga steaming Amachiza matenda monga zifuwa komaso khunyu.
☑️nthangala za mtengou amapangila mafuta omwe amathandizaso ku matenda ambiri monga zotupa, kupweteka KWA mma joint ,achina gout ,kuyabwa mthupi, komaso matenda opasilana pogonana achina chindoko Ndi chizonono Ndi azinzao
👉🏾The root bark is used to relieve the spasms of infantile tetanus and is used for sores, dysentery and jaundice.
👉🏾The juice of the roots is applied to boils and pimples
🪀Mizu ya mtengou imachiza matenda monga kamwazi, jaundice komaso kuzola kumaso ziphuphu zimatha.
🍑Sinjani masamba ake nkupanga juice ndipo muzimwa madzi akewo .
🍑Mizu nayo chimozi mozi isinjeni nkuviika nkumawaadzi ake kapena kupaka pazotupa Ngakhale ziphuphu .
🍑Khungwa lake naloso mmasinja madzi akewo nkumamwa komaso nthangala amazigaya nkupanga powder.
0992449442/0884564513
🌽🥕🫒🧄🥔🍊🍠🍍🍓🍇🍉🍌🍋🍑🍎🍏🫑🌶️🥒🥝🥬🥦🫛🥑🍆🍅🥥🥭🍒🍐🍈🫐🧅