14/04/2026
Pamudzi pano sitilaula kma timaphunzitsa,kudziwitsa,kuchenjeza komanso kupewetsa ndikudzikodzekeletsa pa mavuto osiyanasiyana okhudza dziwalo za thupi lathu,
Ambiri amalephera kupita kuchipatala kuti akathandidzidwe moyenera chifukwa cha manyazi popeza nthenda yagwira malo osaenera.
Please don't be shy panthawi imene mkufunika nnthandizo,
Paja pali mwambi wakuti ikavutika imadya udzu,ndibwno kuvomeleza mmene zinthu zilili kusiyana ndikuti mufe chifukwa chamantha.
Anthu ambir amaona ngati kutchula ziwalo zobisika ndikulaula,ai kulawula kumachitika ngati munthu akutchula zithu zimenezi padzifukwa zosamveka komanso mnjira yongofuna kusangalatsa anthu,kunyodzetsa ndikunyogodola.
Zimenezi zikusiyana ndi cholinga chathu,,
Ife ndikuphunzitsa,kudzudzula,kudziwitsa,kuzindikiritsa,kupewetsa,ndikuthandidza anthu kudziwa zomwe angachite akakumana ndi mavuto ena panthupi lawo,uku sikulawula
Dzikomo,