Healthwise with Kittah

Healthwise with Kittah ✓ Registered Pharmacy personnel💊
✓ Professional Health Educator💉
✓ Midwife 🩺

⚠️This page is for Educational purposes only.

Go to the Hospital and Get checked.!! For Inquiries & Partnership:
💌[email protected]
📞0996451756 (Wap only)

27/08/2026

Mauka simatenda opasilana pogonana ngati mmene alili achina Syphilis, gonorrhea etc
check comments

03/08/2026

Mauka Timathana Nawo Chochi
Yeast infection/ Candidiasis

17/06/2026

Azibambo Akumwalira Chifukwa chakusadziwa.
Mu video mu ndafotokoza zokhuza Comit 100, Kifaru 100, Welgra, voltem, elagra, etc..
Mankhwala othaniza kuchipinda.

💪💪💪💪

07/06/2026

Appetito and C-4
Ntchito ya C-4 ndi Appetito

🇿🇲

🤧🙌😂
13/05/2026

🤧🙌😂

Iwenso ??😅😂
13/05/2026

Iwenso ??😅😂

MA EMERGENCY PILLS: 1. Amagwira ntchito mukamwa within 3 days (72 hrs) after S3x.Nde pali ena amatha kugwira ntchito up ...
09/05/2026

MA EMERGENCY PILLS:
1. Amagwira ntchito mukamwa within 3 days (72 hrs) after S3x.
Nde pali ena amatha kugwira ntchito up to 5 days (120) after S3x.

2. Sitimweratu before S3x, Chifukwa chokuti amayamba kugwira ntchito nthawi yomweyo mukamwa, ndye mphamvu imayamba kutsika as time goes.

3. Emergency pill Samachotsa mimba ngati mwamwa muli kale ndi mimba.

4. Samateteza ku ma STIs

Ngati pali mafunso ena alembeni mu comment section.😊
ZIKOMO.

Nde mwati kwabwera kachifuwa kosachidzika ?Nde mkumatanino anzanga ?
09/05/2026

Nde mwati kwabwera kachifuwa kosachidzika ?
Nde mkumatanino anzanga ?

17/04/2026

Munadziwa bwanji kuti LABOUR yayamba, muthamangire kuchipatala ??
Tiphunzitseni mu comment section 👇

15/04/2026

Azibambo iyiyi its a Must muwonere.
How to Support your wife ku Labour ward

Address

Lilongwe
B1

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Healthwise with Kittah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share