Care MW

Care MW WhatsAp+265 999 37 66 52
(3)

careMW󱢏
"Timaphunzitsa kapewedwe ka matenda osiyanasiyana,muli phee kunyumba kwanu"
" ONCE YOU SEE THIS FOLLOW THE PAGE"
"INVANI ZOONA ZOKHUZA KUCHIPATALA "
"KUCHIMAKE KWA UPHUNGU WAKUCHIPATALA "
👉[email protected].

26/08/2026

Pogona thimisan or dim ma bulb kuti musasokeneze hormone ya melatonin ,imene imapangitsa kugona kwabwino.
Goodnight team👐.

26/08/2026

kungolowa ifeyo a care MW ,Ku meeting anvekele ife azachipatala muno ayi anthu onse kutuluka Kodi timalakwa Chan ifeyo😭🙌?

26/08/2026

KOMA NGATI KU HEALTH NDIKOMWE NTCHITO ZIKUSOWA CHONCHI KULIBWANJ KWINAKU? ANTHU AKUKUTA MANO ULENDO UNO🥹,WATERO TOBIAS

📢 MINISTRY OF HEALTH RECRUITMENT UPDATEThe Ministry of Health had promised that recruitment would begin this month, and ...
26/08/2026

📢 MINISTRY OF HEALTH RECRUITMENT UPDATE

The Ministry of Health had promised that recruitment would begin this month, and the process has now started with the announcement of internal vacancies under the National TB and Leprosy Elimination Programme (NTLEP).

This is an encouraging development for health workers who have been waiting for recruitment opportunities. More recruitment opportunities are expected to follow as the Ministry continues with the process.

the only trusted caregiver in Malawi and beyond care MW tag your friend and stay tuned 👀

25/08/2026

📢 PRESS RELEASE

MINISTRY OF HEALTH AND SANITATION
INTERNAL VACANCIES FOR NATIONAL TB AND LEPROSY ELIMINATION PROGRAMME (NTLEP)

25/08/2026

Kodi mukuziwa ? zimatha kutheka kukhala ndi matenda a m' ubongo wekha osaziziwa kumaona ngati uli bwino 😧

25/08/2026

a Malawi ambiri maka omwe anadwalapo matenda opasilana ndiosangalala ndikutulisidwa kwa kathandizidwe kasopano Ka mankhwala 🫡

good morning
25/08/2026

good morning

23/08/2026

kwasala 8 days yokha koma za period zili pati ?🥴 mawa tingopita kuchipatala ma emergency pills Ake anali a expire ndekuti 😫🙌

abwelesa mphatso pofuna kuwakopa adokotala pa nkhan ya DNA test ija 🙌🥴
23/08/2026

abwelesa mphatso pofuna kuwakopa adokotala pa nkhan ya DNA test ija 🙌🥴

Address

Area
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Care MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Care MW:

Shortcuts

Share