Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club

Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club Medical & Healthy
Arts and Entertainment

Dzulo Mkumano wathu unali motele Pa 31 July tili nd Mbuzi party Join Us today πŸ‘‡
17/05/2026

Dzulo Mkumano wathu unali motele

Pa 31 July tili nd Mbuzi party

Join Us today πŸ‘‡

Mwai kwa wa chinyamata aliyense yemwe ali ndi Malotootukura dziko lino. Ma District Information Session aja sanarekezere...
14/05/2026

Mwai kwa wa chinyamata aliyense yemwe ali ndi Maloto
otukura dziko lino.

Ma District Information Session aja sanarekezere panjira.

Bungwe la Nation Youth Council of Malawi(NYCOM) likupitiriza kudziwitsa anyamata komanso kupereka upangiri wa momwe angapindulire ndi thumba la Youth Innovation Fund(YIF). YIF ndi thumba lokwana 2 Billion Kwacha lomwe lakonzedwa ndi Boma la Malawi kudzera ku NYCOM kuti litukule ma bizinesi achinyamata omwe akuganiza mosiyana, mwamakono komanso mopereka chidwi. Kodi muli ku Mangochi, Dedza kapena Ntcheu? Bwerani mudzazimvere nokha.

Lero zili motere

Mmawa (9PM)
Mangochi-Mangochi Community Hall
Dedza -Dedza Youth Center

Masana (1PM)

Ntcheu-Dear Mama Lodge

Kumbukirani kuti National Youth Council of Malawi sikupereka chitandizo cha ndalama kapena zokumwa kwa omwe abwere ku mikumanoyi.





Ministry of Youth, Sports and Culture - Malawi Malawi Government National Planning Commission of Malawi Ministry of Finance-Malawi

More information follow this page and National Youth Council of Malawi Offices

Team Kasalika Ikanakura join us today πŸ‘†more info 0984006130
10/05/2026

Team Kasalika Ikanakura

join us today πŸ‘†
more info 0984006130

join Us today πŸ‘‡
06/05/2026

join Us today πŸ‘‡

Lero pa 02 Mayi 2026, Team Kasalika  inayendera wimbe youth group kuphunzitsana maluso osayanasiyana kms kugawana utheng...
02/05/2026

Lero pa 02 Mayi 2026, Team Kasalika inayendera wimbe youth group
kuphunzitsana maluso osayanasiyana kms kugawana uthenga wa njira zakulera

join us today Mukuchedwa pat?
More info. 0984006130 Wap, Call or textπŸ’₯πŸ’₯πŸ‘‡

25/04/2026

Team Kasalika Today meeting

join us today..

Team Kasalika sikufoka Dzulo pa 24 April 2026 Team Kasalika inakumana kukambilana Zokhudza business. Wachinyamata otsogo...
25/04/2026

Team Kasalika sikufoka

Dzulo pa 24 April 2026 Team Kasalika inakumana kukambilana Zokhudza
business. Wachinyamata otsogora amayenera kukhala nd chochita

Join us today... Leronso Tikumana khalan alendo athu
more inf. 0984006130

18/04/2026

Lero pa 18 April 2026 , Team Kasalika inapanga izi πŸ‘‡

Join us Today πŸ’₯

15/04/2026

Kasalika youth Conner imalimbikitsanso ma luso osiyanasiyana
join us today kt Mukhale ndi mwai ophunzira kms kutenga njira zakulera Mwa ulele πŸ’₯

Team Kasalika πŸ‘‡πŸ’₯join us today 😎
10/04/2026

Team Kasalika πŸ‘‡πŸ’₯

join us today 😎

27/03/2023

Ndmaona ngat Tuno MW nd Mkaladi πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Kasungu, Kasalika
Kasungu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club:

Share