13/08/2026
*TILI PA CAMPAIGN YOTHANA NDI MATENDA OKHUDZA MTIMA PA MTENGO OKAMBILANA;*
*ZIZINDIKIRO ZOKHUDZA MATENDA AMTIMA;*
Dr Phiri
*CHILANI HERBAL ONLINE CLINIC PLUS;*
_CHIPATALA CHANU;_
+265888890685
+265999890685
βπ» Zizindikiro za matenda amtima zingasiyane, koma zomwe zimapezeka komaso zodziwika kwambiri ndi monga:
1. Kupweteka kapena kukanikizika pachifuwa, makamaka pakati pa pachifuwa.
2. Kupuma movutikira kapena kumva ngati mpweya sukukwanira.
3. Mtima kugunda mwachangu, mwamphamvu kapena mosinthasintha.
4. Kutopa kwambiri popanda chifukwa chodziwika bwino zomwe zimapezeka or mwangoyenda kamtunda kochepa.
5. Chizungulire, (kugwa) kapena kukomoka.
6. Kutupa miyendo, akakolo kapena mapazi.
7. Ululu omwe umatha kufalikira kupita ku mkono, ku phewa, msana, khosi kapena nsagwada.
8. Thukuta lochuluka,
9. Nseru kapena kusanza, makamaka ngati pali kupweteka pachifuwa.
β οΈ Ngati mukunva kupweteka kwambiri pachifuwa, kupuma movutikira kwambiri, kukomoka, kapena ululu ukufalikira ku mkono/nsagwada/msana, Pitani kuchipatala mwachangu kapena itanani thandizo ladzidzidzi. Nthawi zina Izi zimatha kukhala matenda okhudza mtima Kapena zingakhale zizindikiro za heart attack.
Kodi muli ndi vuto Kapena matenda Omwe anatsimikizidwa ndi Chipatala okhudza mtima?
Ngati matendawa mulinawo, Ife a *CHILANI HERBAL ONLINE CLINIC PLUS Lilongwe;* Tili pa campaign (kampeni) kusakasaka anthu odwala matendawa kuti tithandizane nawo popeza Machilitso pa mtengo okambilana;
Bwelani ku Inbox ya *Dr Phiri;* +265888890685 ngati mukufuna Machilitso amatendawa mwansanga
Campaign yathu ikulekeza pa August 31 2026, Watsala watsala, wachila wachila pa mtengo okambilana Normal price ya matendawa ndi K300,000, Uwu ndi mtengo Omwe Timagwilitsa ntchito nthawi zonse
Koma tikuti panopa Tili pa mtengo okambilana kulekeza August 31, Musaphweketse Tili ndi mankhwala amphanvu Omwe akuchiza matendawa Kwa masiku ochepa;
Tipezeni kuno ku Lilongwe, Omwe muli kutali Imbani phone Ndipo mudzathandizidwa;
Kodi mungakonde mutakhala m,modzi wa ma members athu ku ma group athu a Whatsapp? Pitani pa link yathu pansipa ndikutsatila zonse zofunikila kuti mupezeke pa limodzi la ma Whatsapp group athu;
ππ»ππ»
https://chat.whatsapp.com/Iwl4rbtvjWJIT2BXUiyoWp?s=cl&p=a&ilr=4
*Call Or Whatsapp;*
+265888890685
+265999890685