21/06/2026
Before buying antibiotics for a cough, flu, sore throat, or chest infection, talk to a qualified health professional first. Not every respiratory illness needs antibiotics—many are caused by viruses and should be treated differently. Teleconsultation helps you get the right advice, the right treatment, and protects all of us from antibiotic resistance.
Consult first. Treat right. Protect your health. 💙📱💊
Musanagule maantibayotiki chifukwa cha chifuwa, chimfine, kupweteka kwa mmero kapena matenda a m’chipumu, muyenera kaye kulankhula ndi akatswiri azaumoyo kudzera pa teleconsultation. Si matenda onse a m’mapapo kapena m’njira yopumira amene amafuna maantibayotiki—ambiri amayambitsidwa ndi ma virus ndipo amafunikira chithandizo chosiyana.
Teleconsultation imakuthandizani kupeza malangizo oyenera, mankhwala oyenera, komanso kuteteza tonse ku vuto la antibiotic resistance.
Funsani kaye. Landirani chithandizo choyenera. Tetezani thanzi lanu. 💙📱💊